- The Noble Quran
- Sunnah of Prophet Muhammad
- Islamic Creed
- Tawhid (Monotheism)
- Worship
- Islam
- Imān (Faith)
- Matters of Faith
- Benevolence
- Disbelief (Infidelity)
- Hypocrisy
- Shirk (Polytheism)
- Religious Innovation: Types and Examples
- Companions and Family of Prophet Muhammad
- Tawassul (Solicitation)
- The Concept of the Miraculous Acts Done by Some Righteous People
- Jinn
- Loyalty and Friendship vs Disavowal and Enmity
- Ahl-us-Sunnah wa al-Jama‘ah
- Doctrines and Religions
- Sects
- Attributed Sects to Islam
- Contemporary Ideological Doctrines
- Islamic Jurisprudence
- Acts of Worship
- Purification and its Rulings
- Prayer
- Rulings of Funeral
- Zakah
- Fasting
- Pilgrimage and Umrah
- Friday Sermon
- Prayer of the Sick
- Prayer of the Traveler
- Prayer during Fear
- Transactions
- Oaths and Vows
- Family
- Marriage
- Divorce
- Recommended and Disliked Divorce
- Revocable and Irrevocable Divorce
- Woman’s Waiting Period
- Li‘ān (Husband Swearing His Wife Had Intercourse with Another Man)
- Zihār (Likening One’s Wife to His Mother; To Prevent Her On Himself)
- ilā’ (Swearing Not to Intercourse with One's Wife)
- Wife Seeking Divorce
- Taking back One's Divorced Wife
- Breastfeeding
- Child's Custody
- Alimony
- Clothes and Adornment
- Entertainment
- Muslim Society
- Youth Affairs
- Women Affairs
- Children Affairs
- Medicine and Treatment and Islamic Faith-Healing
- Foods and Drinks
- Islamic Criminal Law
- Judiciary System in Islam
- Jihad
- Fiqh of Contemporary Issues
- Fiqh of Minorities
- Islamic Policy
- Schools of Islamic Jurisprudence
- Fatāwa (Fatwas)
- Fundamentals of Islamic Jurisprudence
- Books on Islamic Jurisprudence
- Acts of Worship
- Virtues/Noble Characteristics
- Arabic Language
- Calling to Allah's Religion
- Issues That Muslims Need to Know
- Softening Hearts Reminders
- Promotion of Virtue and Prevention of Vice
- Current State of Calling to Allah's Religion
- chiCheŵa Author : Sheikh Muhammadi Abdul-Hamid Silika
Ndithu matamando onse ndi a Allah, tikumutamanda, kumpempha chithandizo ndi kumpempha chikhululuko, komanso tikuzichinjiriza mwa Allah ku zoyipa za mitima ndi ntchito zathu. Amene Allah wamuongola palibe angamusocheretse, ndipo amene wasochera palibe angamuongole. Ndikuchitira umboni kuti palibe mulungu wina (woyenera kupembedzedwa) koma Allah, Wayekha, wopanda wothandizana naye. Ndikuchitiranso umboni kuti Muhammadi ndikapolo wake komanso mtumiki wake. Adamtumidza ndi chiongoko kudzanso chipembedzo chowona kuti achiyike pamwamba pa zipembedzo zonse ngakhale opembedza mafano ziwanyanse. Pambuyo pa izi: Uku ndiko kutsindikiza koyamba kwa buku la Chikhulupiriro cha Chisilamu, lomwe ndikulipereka kwa anthu a dziko lonse. Buku limeneli ndi zipatso za mapologalamu a Tauhidi omwe ndakhala ndikulalika pa Radio Islam kwa zaka zambiri. Ndipo ndaligawa magawo awiri. Mu gawo loyamba ndakambamo za Tauhidi mmene iliri mu Qur’an ndi Sunnah. Posonkhanitsa ziphunzitso zake ndayazamira buku la Aqidah lomwe lidalembedwa ndi gulu la masheikh omwe ndi akadaulo pa maphunziro a Tauhidi ochokera pa sukulu ya ukachenjede ya Chisilamu ya ku Madinatu Munawwara, komanso sukulu ya ukachenjede ya Chisilamu ya Imam Muhammadi Ibn Saudi mdziko la Saudi Arabia. Mu gawo lachiwiri ndakambamo za Tauhidi mmene iliri mu Baibulo. Posonkhanitsa ziphunzitso zake ndayazamira buku la Mukhtaŝar Kitāb Iđ’hār Al-Haqq lomwe lidalembedwa ndi Sheikh Rahmatu Allah Al-Hindi (Allah awachitire chifundo). Pali masheikh omwe awunika bukuli ndi kuvomereza kuti liri bwino. Iwo ndi: Sheikh Ahmad Chienda, Sheikh Omar Adam Nkachelenga, Sheikh Faruq Jum’a Chibaya ndi Sheikh Dr. Salmin Omar Idrus. Sheikh Muhammadi Abdul-Hamid Silika Al-Madani
- chiCheŵa